Joshua 4:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Miyala imeneyi idzakhala chikumbutso, ndipo anthu azidzakumbukira zimene Chauta wachita. Ana anu akamadzakufunsani m'tsogolo muno tanthauzo lake la miyala imeneyi,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti ichi chikhale chizindikiro pakati pa inu. Akakufunsani ana anu m'tsogolomo, ndi kuti, Miyala iyi nja chiyani ndi inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti ikhale chizindikiro kwa inu. Mʼtsogolo muno ana anu akamadzakufunsani kuti, ‘Kodi miyala iyi ikutanthauza chiyani?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti ici cikhale cizindikilo pakati pa inu. Akakufunsani ana anu m'tsogolomo, ndi kuti, Miyala iyi nja ciani ndi inu?