Joshua 5:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ana ao amene adaloŵa m'malo mwao, sadaumbalidwe pamene anali paulendo m'chipululumo, ndipo ndiwo amene Yoswa adalamula kuti aumbalidwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ana ao amuna amene anawautsa m'malo mwao, iwowa Yoswa anawadula; popeza anakhala osadulidwa, pakuti sanawadule panjira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ana awo amene analowa mʼmalo mwawo ndiwo amene Yoswa anawachita mdulidwe popeza sanachite pamene anali pa ulendo wawo mʼchipululu muja.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ana ao amuna amene anawautsa m'malo mwao, iwowa Yoswa anawadula; popeza anakhala osadulidwa, pakuti sanawadula panjira.