Joshua 6:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adauza anthu kuti, “Yambamponi. Yendani mozungulira mzindawo, ankhondo akhale patsogolo pa Bokosi lachipangano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nati kwa anthu, Pitani, muzizungulira mudzi, ndi ankhondo ndi zida zao atsogolere likasa la Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo analamulira anthu kuti, “Yambani kuyenda! Yendani mozungulira mzinda ndipo ankhondo akhale patsogolo pa Bokosi la Yehova.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nati kwa anthu, Pitani, muzizungulira mudzi, ndi ankhondo ndi zida zao atsogolere likasa la Yehova.