Joshua 7:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adamuuza Yoswa kuti, “Dzuka, chifukwa chiyani wagwada pansi chotere?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, Tauka, wagweranji pankhope pako chotere?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova anati kwa Yoswa, “Imirira! Chifukwa chiyani wagwada pansi chotere?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, Tauka, wagweranji pankhope pako cotere?