Joshua 7:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akani adayankha kuti, “Indedi, ine ndidachimwa, ndidachimwira Chauta, Mulungu wa Aisraele, ndipo zimene ndidachita ndi izi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Akani anayankha Yoswa nati, Zoonadi, ndachimwira Yehova Mulungu wa Israele, ndachita zakutizakuti;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akani anayankha kuti, “Zoona! Ine ndachimwira Yehova Mulungu wa Israeli. Chimene ndachita ine ndi ichi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Akani anayankha Yoswa nati, Zoonadi, ndacimwira Yehova Mulungu wa Israyeli, ndacita zakuti zakuti;