Joshua 7:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yoswa adatuma anthu ena kuti apite kuchithandoko, ndipo adakapezadi kuti zonsezo adazibisa kumeneko, ndipo kuti silivayo adamubisadi pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Yoswa anatuma mithenga, iwo nathamangira kuhema; ndipo taonani, zidabisika m'hema mwake ndi siliva pansi pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero Yoswa anatuma anthu, ndipo anathamanga kupita ku tenti. Anthuwo anakapeza kuti zinthuzo zinabisidwadi mʼtenti yake, ndipo siliva analidi pansi pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Yoswa anatuma mithenga, iwo nathamangira kuhema; ndipo taonani, zidabisika m'hema mwace ndi siliva pansi pace.