Joshua 7:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yoswa adangotuma anthu ngati zikwi zitatu. Koma tsono anthu a ku Ai adapirikitsa Aisraelewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero mwa anthu anakwerako amuna monga zikwi zitatu; koma anathawa pamaso pa amuna a ku Ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho kunapita anthu 3,000. Koma iwo anathamangitsidwa ndi anthu a ku Ai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero mwa anthu anakwerako amuna monga zikwi zitatu; koma anathawa pamaso pa amuna a ku Ai.