Joshua 8:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mamaŵa, Yoswa adadzuka naitana ankhondo ake onse. Tsono iyeyo ndi atsogoleri a Aisraele, adapita ku Ai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa analawira m'mamawa, nayesa anthu, nakwera, iye ndi akulu a Israele, pamaso pa anthu a ku Ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mmawa mwake, Yoswa anadzuka nayitana asilikali ake. Tsono iye pamodzi ndi akuluakulu a Aisraeli anatsogola kupita ku Ai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa analawira mamawa, nayesa anthu, nakwera, iye ndi akuru a Israyeli, pamaso pa anthu a ku Ai.