Joshua 8:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankhondo omwe anali ndi iyeyo adatsogolako, nakamanga zithando chakumpoto kupenyana ndi chipata cha mzindawo. Pakati pa iwowo ndi mzinda wa Aiwo panali chigwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi anthu onse a nkhondo okhala naye anakwera, nayandikira nafika pamaso pa mudzi, namanga misasa kumpoto kwa Ai; koma pakati pa iye ndi Ai panali chigwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Gulu lonse la nkhondo limene linali ndi iye linatsogolako ndi kukamanga zithando pafupi ndi mzindawo chakumpoto mopenyana nawo. Pakati pa iwo ndi mzindawo panali chigwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi anthu onse a nkhondo okhala naye anakwera, nayandikira nafika pamaso pa mudzi, namanga misasa kumpoto kwa Ai; koma pakati pa iye ndi Ai panali cigwa.