Joshua 8:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa adapatula anthu zikwi zisanu, naŵabisa cha kuzambwe kwa mzindawo, pakati pa Ai ndi Betele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenga amuna ngati zikwi zisanu, nawaika m'molalira pakati pa Betele ndi Ai, kumadzulo kwa mudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa anali atatenga asilikali 5,000 ndi kuwabisa pakati pa Ai ndi Beteli, kumadzulo kwa mzindawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenga amuna ngati zikwi zisanu, nawaika m'molalira pakati pa Beteli ndi Ai, kumadzulo kwa mudzi.