Joshua 8:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa pamodzi ndi anthu akewo adachita ngati akuthaŵa, kumaloŵera chakuthengo ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa ndi Aisraele onse anaoneka ngati a ku Ai alikuwathyola, nathawira njira ya kuchipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa ndi Aisraeli onse anachita ngati agonja ndi kumathawira ku chipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa ndi Aisrayeli onse anaoneka ngati a ku Ai alikuwathyola, nathawira njira ya kucipululu.