Joshua 8:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onse amumzindamo adauzidwa kuti aŵatsate pambuyo, ndipo pamene ankapirikitsa Yoswa, iyeyo ankathaŵira kutsogolo ndithu, kutalikirana ndi mzinda wao uja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anthu onse okhala m'mudzi, anaitanidwa awapirikitse, nampirikitsa Yoswa, nakokedwa kusiyana ndi mudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse a ku Ai anawuzidwa kuti awapirikitse. Ndipo iwo anapirikitsadi Yoswa uja, ndi kupita kutali ndi mzinda wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anthu onse okhala m'mudzi, anaitanidwa awapitikitse, nampitikitsa Yoswa, nakokedwa kusiyana ndi mudzi.