Joshua 8:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atangokweza dzanja lake, anthu amene adabisala aja, adavumbuluka msangamsanga, adathamangira mu mzindawo naugonjetsa, ndipo adautentha pomwepo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nauka msanga olalirawo m'mbuto mwao, nathamanga pamene anatambasula dzanja lake, nalowa m'mudzi, naugwira; nafulumira nayatsa mudziwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atangotambalitsa dzanja lake, anthu amene anabisala aja ananyamuka msangamsanga pamalo pawo ndi kuthamangira kutsogolo. Iwo analowa mu mzindamo ndi kuwulanda ndipo anawutentha mofulumira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nauka msanga olalirawo m'mbuto mwao, nathamanga pamene anatambasula dzanja lace, nalowa m'mudzi, naugwira; nafulumira nayatsa mudziwo.