Joshua 8:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palibe ndi mmodzi yemwe amene adapulumuka kapena kutulukamo wamoyo, koma mfumu ya ku Ai yokha. Mfumuyo adaigwira, napita nayo kwa Yoswa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mfumu ya ku Ai anamgwira wamoyo, nadza naye kwa Yoswa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kupatula mfumu ya ku Ai yokha imene anayigwira nabwera nayo kwa Yoswa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mfumu ya ku Ai anamgwira wamoyo, nadza naye kwa Yoswa.