Joshua 8:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chiŵerengero chonse cha anthu a ku Ai amene adaphedwa pa tsikulo chinali zikwi khumi ndi ziŵiri, amuna ndi akazi omwe pamodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo onse amene adagwa tsiku lija, amuna ndi akazi, ndiwo zikwi khumi ndi ziwiri, anthu onse a ku Ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chiwerengero cha anthu onse a ku Ai, amuna ndi akazi, amene anaphedwa pa tsiku limeneli chinali 12,000.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo onse amene adagwa tsiku lija, amuna ndi akazi, ndiwo zikwi khumi ndi ziwiri, anthu onse a ku Ai.