Joshua 8:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa ankalozabe mkondo wake uja ku Ai, osatsitsa dzanja lake mpaka munthu aliyense mumzindamo ataphedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza Yoswa sanabweze dzanja lake limene anatambasula nalo nthungo, mpaka ataononga konse nzika zonse za ku Ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa sanatsitse dzanja lake limene ananyamula mkondo mpaka ataona kuti onse amene amakhala mu mzinda wa Ai aphedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza Yoswa sanabweza dzanja lace limene anatambasula nalo nthungo, mpaka ataononga konse nzika zonse za ku Ai.