Joshua 8:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Aisraele adatenga zoŵeta ndi katundu yense wamumzindawo, monga momwe Chauta adauzira Yoswa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ng'ombe ndi zofunkha za mudzi uwu Israele anadzifunkhira monga mwa mau a Yehova amene analamulira Yoswa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Aisraeli anatenga zoweta ndi katundu yense wa anthu ophedwa aja, monga momwe Yehova analamulira Yoswa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ng'ombe ndi zofunkha za mudzi uwu Israyeli anadzifunkhira monga mwa mau a Yehova amene analamulira Yoswa.