Joshua 8:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pomwepo Yoswa adautentha mzinda wa Ai, nausiya bwinja monga uliri leromu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anatentha Ai, nausandutsa muunda ku nthawi yonse, bwinja kufikira lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Yoswa anawutentha mzinda wa Ai ndi kuwusiya bwinja monga ulili leromu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anatentha Ai, nausandutsa muunda ku nthawi yonse, bwinja kufikira lero lino.