Joshua 8:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yoswa adakonzeka ndi ankhondo ake kupita ku Ai. Adasankhula ankhondo ena olimba mtima zikwi makumi atatu, ndipo adaŵatuma usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anauka Yoswa, ndi anthu onse a nkhondo, kuti akwere ku Ai; ndipo Yoswa anasankha amuna zikwi makumi atatu, ndiwo ngwazi, nawatumiza apite usiku,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Yoswa ndi gulu lonse la nkhondo anakonzeka kupita ku Ai. Iye anasankha amuna 30,000 odziwa kumenya nkhondo bwino ndipo anawatumiza usiku
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anauka Yoswa, ndi anthu onse a nkhondo, kuti akwere ku Ai; ndipo Yoswa anasankha amuna zikwi makumi atatu, ndiwo ngwazi, nawatumiza apite usiku,