Joshua 8:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵapatsa malamulo akuti, “Kabisaleni kumbuyo kwa mzindawo. Musakapite patali ndi mzindawo, koma kakhaleni okonzekera kuuthira nkhondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nawalamulira ndi kuti, Taonani, muzikhala olalira kukhonde kwa mudzi; musakhalira kutali ndi mudzi, koma mukhale okonzekeratu nonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nawapatsa malamulo awa kuti, “Mvetsani bwino; mukabisale kuseri kwa mzindawo. Musakapite patali ndi mzindawo, koma nonsenu mukakhale okonzekera nkhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nawalamulira ndi kuti, Taonani, muzikhala olalira kukhonde kwa mudzi; musakhalira kutali ndi mudzi, koma mukhale okonzekeratu nonse;