Joshua 8:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu anga pamodzi ndi ine ndiye tidzayambe kuuputa mzindawo cha kumaso kwake. Tsono akadzangotuluka kuti alimbane nafe, ife tidzabwerera m'mbuyo, monga momwe tidachitira tsiku lina lija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ine, ndi anthu onse ali nane, tidzayandikira mudzi; ndipo kudzali, pamene atuluka kudzakomana nafe, monga poyamba paja, tidzathawa pamaso pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndi gulu langa lonse tikayamba kuwuputa mzindawu, ndipo akadzangotuluka kudzalimbana nafe, ife tidzawathawa monga tinachitira poyamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ine, ndi anthu onse ali nane, tidzayandikira mudzi; ndipo kudzali, pamene aturuka kudzakomana nafe, monga poyamba paja, tidzathawa pamaso pao;