Joshua 8:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzatithamangitsa motero, mpaka ife titaona kuti ali kutali ndi mzindawo, chifukwa iwowo azidzati, ‘Akutithaŵa monga kale lija.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo adzatuluka kutitsata mpaka tidawakokera asiyane ndi mudzi; pakuti adzanena, Atithawa pamaso pathu monga poyamba paja; nafenso tidzathawa pamaso pao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo adzatithamangitsa mpaka titawakokera kutali ndi mzindawo, pakuti iwo adzati, ‘Akutithawa monga anachitira poyamba.’ Pamene ife tizidzathawa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo adzaturuka kutitsata mpaka tidawakokera asiyane ndi mudzi; pakuti adzanena, Atithawa pamaso pathu monga poyamba pala; nafenso tidzathawa pamaso pao;