Joshua 8:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yoswa adaŵatuma, ndipo iwo adapita ku malo obisalakowo kukaulalira mzindawo. Malowo anali cha kuzambwe kwa Ai, pakati pa Ai ndi Betele. Koma Yoswa ndi gulu lake lankhondo adakhala m'zithando usiku wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anawatuma, namuka iwo kulowa m'molalira, nakhala pakati pa Betele ndi Ai, kumadzulo kwa Ai; koma Yoswa anakhala mwa anthu usiku uja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yoswa atawatumiza, anapita ku malo wokabisalakowo ndipo anadikirira kumeneko. Malowa anali pakati pa Beteli ndi Ai, kumadzulo kwa Ai. Koma Yoswa anagona usiku umenewu pakati pa gulu lake lankhondo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anawatuma, namuka iwo kulowa m'molalira, nakhala pakati pa Beteli ndi Ai, kumadzulo kwa Ai; koma Yoswa anakhala mwa anthu usiku uja.