Joshua 9:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndiponso zimene adachita kwa mafumu aŵiri a Aamori kuvuma kwa Yordani, kwa Sihoni mfumu ya ku Hesiboni, ndiponso kwa Ogi, mfumu ya ku Basani, imene imakhala ku Asitaroti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zonse anachitira mafumu awiri a Aamori okhala tsidya lija la Yordani, Sihoni mfumu ya ku Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya ku Basani wokhala ku Asitaroti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi zonse zimene anachita kwa mafumu awiri a Aamori kummawa kwa Yorodani, mfumu Sihoni ya Hesiboni ndi Ogi mfumu ya Basani amene amalamulira ku Asiteroti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zonse anacitira mafumu awiri a Aamori okhala tsidya lija la Yordano, Sihoni mfumu ya ku Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya ku Basana wokhala ku Asitorotu.