Joshua 9:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono atsogoleri athu ndi anthu onse okhala m'dziko lathu adatiwuza kuti, ‘Konzani chakudya chapaulendo, pitani mukakumane nawo anthu amenewo ndipo mukanene kuti, “Ife tadzagonja, chonde mupangane nafe zamtendere.” ’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akulu athu ndi nzika zonse za m'dziko mwathu zidanena nafe ndi kuti, Mutenge m'dzanja lanu kamba wa paulendo, kakomane naoni, nimunene nao, Ndife akapolo anu; ndipo tsopano mupangane nafe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono akuluakulu athu ndi onse amene akukhala mʼdziko lathu anati kwa ife. Tengani chakudya cha pa ulendo wanu. Pitani mukakumane nawo ndipo mukati kwa iwo, ‘Ife ndife akapolo anu, ndipo tikufuna kuti mugwirizane nafe za mtendere.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akuru athu ndi nzika zonse za m'dziko mwathu zidanena nafe ndi kuti, Mutenge m'dzanja lanu kamba wa paulendo, kakomane naoni, nimunene nao, Ndife akapolo anu; ndipo tsopano mupangane nafe.