Joshua 9:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene tinali kuthira vinyo, matumbaŵa anali atsopano ndithu, koma taonani ngong'ambika. Zovala zathu ndi nsapatozi zangokhala nsanza zokhazokha, chifukwa cha kutalika kwa ulendo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi matumba a vinyo awa tinawadzaza akali atsopano; ndipo taonani, ang'ambika; ndi malaya athu awa ndi nsapato zathu zatha, chifukwa cha ulendo wochokera kutali ndithu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zikopa zimene tinathiramo vinyozi zinali zatsopano, koma taonani zathetheka. Zovala zathu ndi nsapato zathu zatha chifukwa cha kutalika kwa ulendo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi matumba a vinyo awa tinawadzaza akali atsopano; ndipo taonani, ang'ambika; ndi malaya athu awa ndi nsapato zathu zatha, cifukwa ca ulendo wocokera kutali ndithu.