Joshua 9:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Aisraele adachoka napita kwao kwa anthuwo, napeza kuti mizinda yao inali Gibiyoni, Kefira, Beeroti ndi Kiriyati-Yearimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, nafika kumidzi yao tsiku lachitatu. Koma midzi yao ndiyo Gibiyoni, ndi Kefira, ndi Beeroti ndi Kiriyati-Yearimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Aisraeli ananyamuka ulendo ndipo tsiku lachitatu anafika ku mizinda ya Gibiyoni, Kefira, Beeroti ndi Kiriati-Yearimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli anayenda ulendo, nafika ku midzi yap tsiku lacitatu. Koma midzi yao ndiyo Gibeoni, ndi Cefira, ndi Beerotu ndi KiriyatuYearimu.