Joshua 9:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma atsogoleriwo adayankha kuti, “Ife tidaŵalonjeza m'dzina la Chauta, Mulungu wa Aisraele, ndipo tsopano sitingathe kuŵapha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akalonga onse ananena kwa msonkhano wonse, Tinawalumbirira kwa Yehova Mulungu wa Israele, m'mwemo sitikhoza kuwachitira kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma atsogoleriwo anayankha kuti, “Ife tinawalonjeza mʼdzina la Yehova, Mulungu wa Israeli, ndipo tsopano sitingawaphe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akalonga onse ananena kwa msonkhano wonse, Tinawalumbirira kwa Yehova Mulungu wa Israyeli, m'mwemo sitikhoza kuwacitira kanthu.