Joshua 9:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndiye onseŵa adapangana za kulimbana ndi Yoswa ndi Aisraele onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anasonkhana kuponyana ndi Yoswa ndi Israele, ndi mtima umodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
anapangana kuti achite nkhondo ndi Yoswa ndi Israeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
anasonkhana kuponyana ndi Yoswa ndi Israyeli, ndi mtima umodzi.