Joshua 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tiŵalole akhale moyo, kuti ukali wa Mulungu ungatigwere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tidzawachitira ichi, ndi kuwasunga amoyo; ungatigwere mkwiyo chifukwa cha lumbirolo tidawalumbirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimene tidzachita nawo ndi ichi: Tidzawasiya akhale ndi moyo kuti mkwiyo wa Yehova usatigwere chifukwa chophwanya lonjezo limene tinawalonjeza.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tidzawacitira ici, ndi kuwasunga amoyo; ungatigwere mkwiyo cifukwa ca lumbirolo tidawalumbirira.