Joshua 9:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alekeni akhale moyo, komatu azitidulira nkhuni ndi kumatitungiranso madzi.” Zimenezi ndizo zimene adanena atsogoleri aja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akalonga ananena nao, Akhale ndi moyo; ndipo anasanduka akutema nkhuni, ndi otungira madzi msonkhano wonse; monga akalonga adanena nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapitiriza kunena kuti “Asiyeni akhale ndi moyo, komabe akhale otidulira mitengo ndi kutitungira madzi ogwiritsa ntchito pa chipembedzo.” Lonjezo la atsogoleriwo linasungidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akalonga ananena nao, Akhale ndi moyo; ndipo anasanduka akutema nkhuni, ndi otungira madzi msonkhano wonse; monga akalonga adanena nao.