Joshua 9:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yoswa adaŵaitana Agibiyoniwo, naŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mudatinyenga potiwuza kuti mwachokera kutali, chikhalirecho ndinu a pafupi pompano?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yoswa anawaitana, nanena nao, kuti, Mwatinyenga chifukwa ninji, ndi kuti, Tikhala kutalitali ndi inu, pokhala kwanu kuli pakati pa ife?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yoswa anayitanitsa Agibiyoni aja nawafunsa kuti, “Chifukwa chiyani inu munatinyenga ponena kuti mumachokera kutali pamene zoona zake nʼzoti mumakhala pafupi pomwe pano?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yoswa anawaitana, nanena nao, kuti, Mwatinyenga cifukwa ninji, ndi kuti, Tikhala kutaritari ndi inu, pokhala kwanu kuli pakati pa ife?