Joshua 9:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Yoswa adaŵatchinjiriza anthuwo, kuti Aisraele angaŵachite zoipa, kapena kuŵapha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anawachitira chotero, nawalanditsa m'dzanja la ana a Israele, angawaphe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yoswa anawapulumutsa mʼmanja mwa Aisraeli ndipo sanawaphe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anawacitira cotero, nawalanditsa m'dzanja la ana a Israyeli, angawaphe.