Joshua 9:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Ahivi a ku Gibiyoni atamva zimene Yoswa adaachita mzinda wa Yeriko ndi wa Ai,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene nzika za Gibiyoni zinamva zimene Yoswa adachitira Yeriko ndi Ai,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Ahivi ena a ku Gibiyoni atamva zomwe Yoswa anachitira mizinda ya Yeriko ndi Ai,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene nzika za Gibeoni zinamva zimene Yoswa adacitira Yeriko ndi Ai,