Joshua 9:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adapita kwa Yoswa ku zithando ku Giligala kuja, namuuza iyeyo pamodzi ndi Aisraele onse kuti, “Ife tachoka ku dziko lakutali, ndipo tikufuna kuti tichite nanu chipangano.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zinamuka kwa Yoswa kumisasa ku Giligala, niziti kwa iye ndi kwa amuna a Israele, Tachokera dziko lakutali, chifukwa chake mupangane nafe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anapita kwa Yoswa ku msasa ku Giligala ndikumuwuza kuti, pamodzi ndi Aisraeli onse, “Ife tachokera ku dziko lakutali, ndipo tikufuna kuti muchite mgwirizano ndi ife.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zinamuka kwa Yoswa kumisasa ku Giligala, niziti kwa iye ndi kwa amuna a Israyeli, Tacokera dziko lakutali, cifukwa cace mupangane nafe.