Joshua 9:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Aisraele adayankha kuti, “Mwina mwake kwanu nkufupi konkuno. Nanga tingachite nanu chipangano bwanji?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo amuna a Israele anati kwa Ahivi, Kapena mulimkukhala pakati pa ife, ndipo tipanganenji ndi inu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Aisraeli anayankha Ahiviwo kuti, “Mwinatu inu mukukhala pafupi ndi ife. Tsono ife tingachite bwanji mgwirizano ndi inu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo amuna a Israyeli anati kwa Ahivi, Kapena mulimkukhala pakati pa ife, ndipo tipanganenji ndi inu?