Joshua 9:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adauza Yoswa kuti, “Ife ndife akapolo anu.” Tsono Yoswa adaŵafunsa kuti, “Kodi inu ndinu yani? Mwachoka kuti?” Anthuwo adamuuza nkhani yonse, adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anati kwa Yoswa, Ndife akapolo anu. Pamenepo Yoswa anati kwa iwo, Ndinu ayani? Ndipo mufuma kuti?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anati kwa Yoswa, “Ife ndife akapolo anu.” Tsono Yoswa anawafunsa kuti, “Inu ndinu yani ndipo mukuchokera kuti?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anati kwa Yoswa, Ndife akapolo anu. Pamenepo Yoswa anati kwa iwo, Ndinu ayani? ndipo mufuma kuti