Jude 1:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Enoki, wa mbadwo wachisanu ndi chiŵiri kuyambira pa Adamu, adaalosa za anthu okhaokhaŵa pamene adati, “Onani, Ambuye akubwera ndi angelo ake osaŵerengeka,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kwa iwo, Enoki, wachisanu ndi chiwiri kuyambira kwa Adamu, ananenera kuti, Taona, wadza Ambuye ndi oyera ake zikwi makumi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Enoki, wachisanu ndi chiwiri kuyambira pa Adamu, ananeneratu za anthu amenewa kuti, “Onani, Ambuye akubwera ndi oyera ake osawerengeka
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kwa iwo, Henoke, wacisanu ndi ciwiri kuyambira kwa Adamu, ananenera kuti, Taona, wadza Ambuye ndi oyera ace zikwi makumi,