Jude 1:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano ndati ndikukumbutseni zina, ngakhale mudazidziŵa kale zonse. Paja Ambuye adaapulumutsa mtundu wa Aisraele ku dziko la Ejipito, koma pambuyo pake adaŵaononga onse amene sadakhulupirire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale, kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwatulutsa m'dziko la Ejipito, anaononganso iwo osakhulupirira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale munazidziwa kale zonsezi, ndafuna kuti ndikukumbutseni kuti Ambuye anapulumutsa anthu ake ndi kuwatulutsa mʼdziko la Igupto, koma pambuyo pake anawononga amene sanakhulupirire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwaturutsa m'dziko La Aigupto, anaononganso iwo osakhulunirira.