Judges 1:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakalimbananso ndi Akanani amene ankakhala ku Hebroni, (mzinda umene kale ankautchula kuti Kiriyati-Ariba). Kumeneko adagonjetsa mabanja a Sesai, Ahimani ndiponso Talimai.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yuda anamuka kwa Akanani akukhala m'Hebroni; koma kale dzina la Hebroni ndilo mudzi wa Ariba; ndipo anakantha Sesai, ndi Ahimani, ndi Talimai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anakalimbananso ndi Akanaani amene ankakhala ku Hebroni (mzinda womwe kale unkatchedwa Kiriyati-Araba). Kumeneko anagonjetsa Sesai, Ahimani ndi Talimai.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yuda anamuka kwa Akanani akukhala m'Hebroni; koma kale dzina la Hebroni ndilo mudzi wa Ariba; ndipo anakantha Sesai, ndi Ahimani, ndi Talimai.