Judges 1:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuchokera kumeneko anthu a ku Yuda aja adapita kukalimbana ndi anthu a ku Debiri. Mzinda umenewu kale unkatchedwa Kiriyati-Sefere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pochoka pamenepo anamuka kwa nzika za ku Debiri, koma kale dzina la Debiri ndilo mudzi wa Kiriyati-Sefere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuchokera kumeneko, iwo anakathira nkhondo anthu amene ankakhala ku Debri (mzindawu poyamba unkatchedwa Kiriati Seferi).
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pocoka pamenepo anamuka kwa nzika za ku Dibiri, koma kale dzina la Dibiri ndilo mudzi wa Seferi.