Judges 1:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ayuda adalandanso mzinda wa Gaza ndi dziko lake lonse lozungulira, Asikeloni ndi dziko lake lonse lozungulira, ndiponso Ekeroni ndi dziko lake lonse lozungulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yuda analandanso Gaza ndi malire ake, ndi Asikeloni ndi malire ake ndi Ekeroni ndi malire ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu a fuko la Yuda analandanso mzinda wa Gaza ndi dziko lonse lozungulira, mzinda wa Asikeloni pamodzi ndi dziko lake lonse lozungulira, ndi mzinda wa Ekroni pamodzi ndi dziko lonse lozungulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yuda analandanso Gaza ndi malire ace, ndi Asikeloni ndi malire ace, ndi Ekroni ndi malire ace.