Judges 1:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adaŵathandiza Ayuda, ndipo Ayudawo adalanda dziko lamapiri, koma sadathe kupirikitsa nzika zam'chigwa, chifukwa chakuti zinali ndi magaleta achitsulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anali ndi Yuda, iye nawaingitsa a kumapiri, osaingitsa nzika za kuchigwa, popeza zinali nao magaleta achitsulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anathandiza anthu a fuko la Yuda. Iwo analanda dziko la kumapiri, koma sanathe kuwachotsa anthu ku zigwa, chifukwa anali ndi magaleta azitsulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anali ndi Yuda, iye nawaingitsa a kumapiri, osaingitsanzika za kucigwa, popeza zinali nao magareta acitsulo.