Judges 1:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatuma anthu oti akazonde Betele, (mzinda umene kale ankautchula Luzi).
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo a m'nyumba ya Yosefe anatumiza ozonda ku Betele. Koma kale dzina la mudziwo ndilo Luzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anatumiza anthu kuti akazonde Beteli. Mzindawo kale unkatchedwa Luzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo a m'nyumba ya Yosefe anatumiza ozonda ku Beteli. Koma kale dzina la mudziwo ndilo Luzi.