Judges 1:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthuyo adaŵasonyeza njira yoloŵera mumzindamo. Iwo aja adapha anthu onse amumzindamo ndi lupanga, koma munthu uja adamleka osamupha, pamodzi ndi banja lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nawaonetsa polowera m'mudzi iye, naukantha mudzi iwowa ndi lupanga lakuthwa; koma analola munthuyo ndi banja lake lonse amuke.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho iye anawaonetsa njirayo, ndipo iwo anapha anthu onse mu mzindamo ndi lupanga koma munthu uja pamodzi ndi banja lake sanawaphe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nawaonetsa polowera m'mudzi iye, naukantha mudzi iwowa ndi lupanga lakuthwa; koma analola munthuyo ndi banja lace lonse amuke.