Judges 1:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Aisraele adasanduka amphamvu, adayamba kuŵagwiritsa Akananiwo ntchito yaukapolo, koma sadaŵapirikitse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo kunali, atakula mphamvu Israele, anasonkhetsa Akanani, osawaingitsa onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeli atakhala amphamvu, anawagwiritsa Akanaaniwo ntchito yakalavulagaga, koma sanawapirikitse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo kunali, atakula mphamvu Israyeli, anasonkhetsa Akanani, osawaingitsa onse.