Judges 1:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aasere sadapirikitse nzika za mu Ako, nzika za mu Sidoni, nzika za mu Alabu, nzika za mu Akizibu, nzika za mu Heliba, nzika za mu Afiki ndiponso nzika za mu Rehobu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Asere sanaingitse nzika za ku Ako, kapena nzika za ku Sidoni, kapena a Alabu, kapena a Akizibu, kapena a Heliba, kapena a Afiki, kapena a Rehobu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
A fuko la Aseri nawo sanathamangitse amene amakhala mu Ako, Sidoni, Ahilabu, Akizibu, Heliba, Afiki, ndi Rehobu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aseri sanaingitsa nzika za ku Ako, kapena nzika za ku Sidoni, kapena a Akalabu, kapena a Akisibu, kapena a Heliba, kapena a Afiki, kapena a Rehobo;