Judges 1:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Aasere adakhala pakati pa Akanani, nzika za dzikolo, pakuti sadaŵapirikitse Akananiwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma Asere anakhala pakati pa Akanani nzika za kudziko; pakuti sanawaingitse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho anthu a fuko la Aseri anakhala pakati pa Akanaani amene ankakhala mʼdzikomo popeza sanawapirikitse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma Aseri anakhala pakati pa Akanani nzika za kudziko; pakuti sanawaingitsa.