Judges 1:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aamori adapirikitsira anthu a fuko la Dani ku dziko lamapiri ndipo sadaŵalole kuti atsikire ku zigwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Aamori anakankha ana a Dani akhale kumapiri pakuti sanawalole atsikire kuchigwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aamori anapirikitsira anthu a fuko la Dani ku dziko la ku mapiri popeza sanawalole kuti atsikire ku chigwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Aamori anakankha ana a Dani akhale kumapiri pakuti sanawalola atsikire kucigwa;