Judges 1:35 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aamori sadachoke koma ankakhalabe ku phiri la Heresi, ku Aiyaloni, ndiponso ku Salibimu. Koma a fuko la Yosefe adasanduka amphamvu, nagwiritsa Aamoriwo ntchito yaukapolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Aamori anakhumbanso kukhala kuphiri la Heresi, ku Ayaloni, ndi ku Saalibimu; koma dzanja la a m'nyumba ya Yosefe linawalaka, nakhala iwo akupereka msonkho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aamori anatsimikiza mtima zokhalabe ku phiri la Hara-Heresi, ku Ayaloni, ndiponso ku Saalibimu. Koma a fuko la Yosefe anakula mphamvu ndipo anagwiritsa Aamoriwo ntchito yakalavulagaga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aamori anakhumbanso kukhala ku phiri la Heresi, ku Ajaloni, ndi ku Saalibimu; koma dzanja la a m'nyumba ya Yosefe linawalaka, nakhala iwo akupereka msonkho.